Skip to content
- Never climb alone. A party of four is ideal.
- Choose a route according to the experience, ability and fitness of the group.
- Use a guidebook or go with someone who genuinely knows the way.
- Ensure that at least one member of the group has a fully charged cell phone.
- Always go prepared for bad weather
- Tell someone where you are going and stick to the plan
- Travel at the pace of the slowest member of the group
- Never split up and go in different directions
- Don’t push on into the unknown. If you get lost retrace your steps.
- If you are unsure of what to do find shelter especially from the wind and stay put.
- Musakwere Phiri nokha. Mukuyenera kukhala anthu anayi
- Sankhani njira yokwerera Phiri yomwe mungayithe malinga ndi luntha lanu komanso ndi mphamvu za gulu lanu.
- Gwirisani tnchito mabuku ofotokoza za momwe mungayendere mu Phiri kapena tengani munthu amene amalondorera anthu mu Phiri ndipo oziwa za Phiri kwambiri.
- Onesesani kuti m’modzi wagulu lanu ali ndi phone yo charger bwino.
- Nthawo zonse khalani okonzeka ukumana ndi nyengo yoyipa ngati yozizira ndipo nyamulani za mphepo.
- Uzani munthu ku malo komwe mukupita ndipo musasinthe.
- Musayende njira zosiyanasiyana pokwera Phiri, yendani limodzi ngati gulu.
- Yendani pa mlingo wa munthu woyenda pang’ono pang’ono pagulu lanulo
- Musapitirire pa njira yoti simukuyiziwa, mukasochera bwererani njira yomwe mwachokera.
- Ngati mwapezana ndi mphepo ya nkuntho, bisalani pamalo abwino ngati simukuziwa chochita.